Tipewe mulili wa Colona – New song about Coronavirus prevention from Jack Allison

Monday October 12, 2020

TIPEWE MULILI wa COLONA: Let’s Prevent the Corona Pandemic

Tiyenera kusunga moyo wathu’wu X2: We must take good care of our lives

Kusunga moyo ndi kofunika: Preserving life is important

Tiyenera kupewa Colona tsiku ndi tsiku: We must prevent Corona every day

Titalikilane mamita awiri pakati pa wina ndi mnzake: We must stay two meters apart from one another

Titaikilane mamita awiri: We must stay two meters apart

kuti tipewe mulili wa Colona: in order to prevent the Corona pandemic

File Attachments
Skip to content